Yeremiya 44:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ine ndikhala tcheru kuti ndiwabweretsere tsoka osati zabwino.+ Ndipo anthu onse a ku Yuda amene ali m’dziko la Iguputo adzafa ndi lupanga ndi njala yaikulu kufikira atatheratu.+
27 Ine ndikhala tcheru kuti ndiwabweretsere tsoka osati zabwino.+ Ndipo anthu onse a ku Yuda amene ali m’dziko la Iguputo adzafa ndi lupanga ndi njala yaikulu kufikira atatheratu.+