Ezekieli 7:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Aliyense akunyada chifukwa cha chinthu chake chokongoletsera. Iwo agwiritsira ntchito siliva ndi golide kupangira mafano awo onyansa,+ ndi zinthu zawo zonyansa.+ N’chifukwa chake ndidzachititse kuti zinthu zimenezi adzaipidwe nazo.+
20 Aliyense akunyada chifukwa cha chinthu chake chokongoletsera. Iwo agwiritsira ntchito siliva ndi golide kupangira mafano awo onyansa,+ ndi zinthu zawo zonyansa.+ N’chifukwa chake ndidzachititse kuti zinthu zimenezi adzaipidwe nazo.+