2 Mbiri 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno anapanga bwalo+ la ansembe+ ndi bwalo lalikulu lamkati+ ndi zitseko za bwalo lalikululo. Zitsekozo anazikuta ndi mkuwa.
9 Ndiyeno anapanga bwalo+ la ansembe+ ndi bwalo lalikulu lamkati+ ndi zitseko za bwalo lalikululo. Zitsekozo anazikuta ndi mkuwa.