Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezekieli 10:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ndinapitiriza kuona masomphenya, ndipo ndinaona kuti pambali pa akerubi panali mawilo anayi. Pambali pa kerubi aliyense panali wilo limodzi.+ Maonekedwe a mawilowo anali ngati kuwala kwa mwala wa kulusolito.

  • Ezekieli 10:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Kenako ndinamva mawu akuitana mawilowo kuti, “Mawilo inu!”

  • Ezekieli 11:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Tsopano akerubi+ aja anatambasula mapiko awo ndipo mawilo anali pambali pawo.+ Ulemerero+ wa Mulungu wa Isiraeli unali pamwamba pa mitu yawo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena