Miyambo 6:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 N’chifukwa chake tsoka lake lidzabwere mwadzidzidzi.+ Adzathyoledwa modzidzimutsa, ndipo sadzachira.+ Machitidwe 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Hananiya atamva mawu amenewa anagwa pansi ndi kumwalira.+ Ndipo onse amene anamva zimenezi anagwidwa ndi mantha aakulu.+
15 N’chifukwa chake tsoka lake lidzabwere mwadzidzidzi.+ Adzathyoledwa modzidzimutsa, ndipo sadzachira.+
5 Hananiya atamva mawu amenewa anagwa pansi ndi kumwalira.+ Ndipo onse amene anamva zimenezi anagwidwa ndi mantha aakulu.+