Salimo 73:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndithudi, mwawaimika pamalo oterera.+Mwawagwetsa kuti awonongeke.+ Miyambo 1:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 zimene mumaopa zikadzabwera ngati mvula yamkuntho, tsoka likadzakufikirani ngati mphepo yamkuntho,+ ndiponso masautso ndi nthawi zovuta zikadzakugwerani.+ Yesaya 30:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pa chifukwa chimenechi, kwa inu cholakwa chanuchi chidzakhala ngati mpanda wautali kwambiri umene wang’aluka penapake n’kupendekeka,+ umene ukhoza kugwa mwadzidzidzi, mosayembekezereka.+ 1 Atesalonika 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pamene azidzati:+ “Bata ndi mtendere!”+ chiwonongeko+ chodzidzimutsa chidzafika pa iwo nthawi yomweyo monga zowawa za pobereka za mkazi wapakati,+ ndipo sadzapulumuka.+
27 zimene mumaopa zikadzabwera ngati mvula yamkuntho, tsoka likadzakufikirani ngati mphepo yamkuntho,+ ndiponso masautso ndi nthawi zovuta zikadzakugwerani.+
13 Pa chifukwa chimenechi, kwa inu cholakwa chanuchi chidzakhala ngati mpanda wautali kwambiri umene wang’aluka penapake n’kupendekeka,+ umene ukhoza kugwa mwadzidzidzi, mosayembekezereka.+
3 Pamene azidzati:+ “Bata ndi mtendere!”+ chiwonongeko+ chodzidzimutsa chidzafika pa iwo nthawi yomweyo monga zowawa za pobereka za mkazi wapakati,+ ndipo sadzapulumuka.+