Ezekieli 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Akerubi akaima chilili, mawilonso anali kuima chilili. Akerubiwo akakwera m’mwamba,+ mawilonso anali kukwera m’mwamba, pakuti mzimu wa zamoyozo unali m’mawilowo.+
17 Akerubi akaima chilili, mawilonso anali kuima chilili. Akerubiwo akakwera m’mwamba,+ mawilonso anali kukwera m’mwamba, pakuti mzimu wa zamoyozo unali m’mawilowo.+