3 Iye anandiuza kuti: “Iwe mwana wa munthu, ndikukutumiza kwa ana a Isiraeli,+ kwa mitundu yopanduka imene yandipandukira.+ Iwo ndi makolo awo akhala akuphwanya malamulo anga mpaka lero.+
26 Ndidzachititsa lilime lako kumatirira kumwamba m’kamwa mwako,+ ndipo sudzathanso kulankhula.+ Sudzakhalanso munthu wowadzudzula,+ pakuti iwo ndi nyumba yopanduka.+