Genesis 9:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndiika utawaleza+ mumtambo, kuti ukhale chizindikiro cha pangano pakati pa ine ndi dziko lapansi. Chivumbulutso 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Wokhala pampandoyo, anali wooneka+ ngati mwala wa yasipi,+ ndi mwala wofiira wamtengo wapatali. Utawaleza+ wooneka ngati mwala wa emarodi+ unazungulira mpando wachifumuwo.
3 Wokhala pampandoyo, anali wooneka+ ngati mwala wa yasipi,+ ndi mwala wofiira wamtengo wapatali. Utawaleza+ wooneka ngati mwala wa emarodi+ unazungulira mpando wachifumuwo.