Ezekieli 8:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iye anandiuza kuti: “Iwe mwana wa munthu, takweza maso ako uyang’ane kumpoto.” Chotero ndinakweza maso anga n’kuyang’ana kumpoto, ndipo ndinaona kuti kumpoto kwa chipata cha guwa lansembe kunali chizindikiro choimira nsanje+ pakhomo la chipatalo. Ezekieli 37:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno anandifunsa kuti: “Iwe mwana wa munthu, kodi mafupa awa angakhale ndi moyo?” Pamenepo ndinayankha kuti: “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, ndinu amene mukudziwa bwino zimenezo.”+
5 Iye anandiuza kuti: “Iwe mwana wa munthu, takweza maso ako uyang’ane kumpoto.” Chotero ndinakweza maso anga n’kuyang’ana kumpoto, ndipo ndinaona kuti kumpoto kwa chipata cha guwa lansembe kunali chizindikiro choimira nsanje+ pakhomo la chipatalo.
3 Ndiyeno anandifunsa kuti: “Iwe mwana wa munthu, kodi mafupa awa angakhale ndi moyo?” Pamenepo ndinayankha kuti: “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, ndinu amene mukudziwa bwino zimenezo.”+