Danieli 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iye anandiuza kuti: “Iwe Danieli, munthu wokondedwa kwambiri,+ mvetsetsa zinthu zimene ndikukuuza+ ndipo uimirire chifukwa ndatumidwa kwa iwe.” Atandiuza zimenezi ndinaimiriradi koma ndikunjenjemera.
11 Iye anandiuza kuti: “Iwe Danieli, munthu wokondedwa kwambiri,+ mvetsetsa zinthu zimene ndikukuuza+ ndipo uimirire chifukwa ndatumidwa kwa iwe.” Atandiuza zimenezi ndinaimiriradi koma ndikunjenjemera.