Ezekieli 16:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Umuuze kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, akunena kwa iwe Yerusalemu kuti: “Iwe unachokera kudziko la Akanani ndipo unabadwira komweko.+ Bambo ako anali Muamori,+ mayi ako anali Mhiti.+
3 Umuuze kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, akunena kwa iwe Yerusalemu kuti: “Iwe unachokera kudziko la Akanani ndipo unabadwira komweko.+ Bambo ako anali Muamori,+ mayi ako anali Mhiti.+