5 “Pakuti Wokupanga Wamkulu+ ndiye mwamuna wako.+ Dzina lake ndi Yehova wa makamu,+ ndipo Woyera wa Isiraeli ndiye Wokuwombola.+ Iye adzatchedwa Mulungu wa dziko lonse lapansi.+
2 Imbani mlandu mayi wanu.+ Muimbeni mlandu pakuti iye si mkazi wanga+ ndipo ine sindine mwamuna wake.+ Mayi wanuyo asiye dama lake ndi chigololo chake,*+