Ezekieli 20:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 “‘Monga mmene ndinatsutsirana ndi makolo anu m’chipululu cha dziko la Iguputo,+ ndidzatsutsananso ndi inu,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa. Mika 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Inu mapiri, imvani mlandu umene Yehova ali nawo pa anthu ake. Inu matanthwe okhazikika, tamverani. Mvetserani inu maziko a dziko lapansi,+ pakuti Yehova ali ndi mlandu ndi anthu ake. Iye azenga mlandu Aisiraeli, kuti:+
36 “‘Monga mmene ndinatsutsirana ndi makolo anu m’chipululu cha dziko la Iguputo,+ ndidzatsutsananso ndi inu,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.
2 Inu mapiri, imvani mlandu umene Yehova ali nawo pa anthu ake. Inu matanthwe okhazikika, tamverani. Mvetserani inu maziko a dziko lapansi,+ pakuti Yehova ali ndi mlandu ndi anthu ake. Iye azenga mlandu Aisiraeli, kuti:+