6 Koma ana a anthu akuphawo sanawaphe, mogwirizana ndi zimene zinalembedwa m’buku la chilamulo cha Mose chimene Yehova analamula. Iye analamula kuti:+ “Abambo asaphedwe chifukwa cha machimo a ana, ndipo ana asaphedwe chifukwa cha machimo a abambo. Aliyense aziphedwa chifukwa cha tchimo lake.”+