-
Danieli 6:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Nduna zonse zapamwamba za mu ufumu uno, akuluakulu a boma, masatarapi, alangizi a mfumu, ndi abwanamkubwa agwirizana kuti inu mfumu mukhazikitse lamulo+ loletsa munthu aliyense kupemphera kwa mulungu kapena kwa munthu wina aliyense kwa masiku 30, kupatulapo kwa inu nokha mfumu. Aliyense amene samvera lamulo limeneli aponyedwe m’dzenje la mikango.+
-