Danieli 5:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Pamenepo Belisazara analamula kuti Danieli amuveke zovala zofiirira ndi mkanda wagolide m’khosi mwake, ndipo analengeza kuti Danieli akhala wolamulira wachitatu mu ufumuwo.+
29 Pamenepo Belisazara analamula kuti Danieli amuveke zovala zofiirira ndi mkanda wagolide m’khosi mwake, ndipo analengeza kuti Danieli akhala wolamulira wachitatu mu ufumuwo.+