7 koma mkulu wa nduna za panyumba ya mfumu anapatsa anawa mayina ena.+ Danieli anamupatsa dzina lakuti Belitesazara,+ Hananiya anamupatsa dzina lakuti Sadirake, Misayeli anamupatsa dzina lakuti Mesake, ndipo Azariya anamupatsa dzina lakuti Abedinego.+