Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Danieli 2:49
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 49 Ndipo Danieli anapempha mfumu kuti iike Sadirake, Mesake ndi Abedinego+ kuti akhale oyang’anira chigawo cha Babulo, ndipo mfumuyo inawaikadi. Koma Danieli anali kutumikira m’nyumba ya mfumu.+

  • Danieli 3:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Koma pali Ayuda ena amene munawaika kukhala oyang’anira chigawo cha Babulo.+ Amuna amphamvu amenewa, Sadirake, Mesake ndi Abedinego, sakukumverani inu mfumu. Iwo sakutumikira milungu yanu ndipo sakulambira fano lagolide limene mwaimika.”+

  • Danieli 3:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Pamenepo Nebukadinezara anati: “Atamandike Mulungu wa Sadirake, Mesake ndi Abedinego+ amene anatumiza mngelo wake+ ndi kupulumutsa atumiki ake amene anamudalira+ ndiponso amene sanamvere mawu a mfumu, koma anali okonzeka kufa chifukwa sanafune kutumikira+ ndi kulambira+ mulungu wina aliyense kupatulapo Mulungu wawo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena