Yesaya 14:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iweyo wanena mumtima mwako kuti, ‘Ndikwera kumwamba.+ Ndikweza mpando wanga wachifumu+ pamwamba pa nyenyezi+ za Mulungu. Ndikhala paphiri lokumanapo+ kumapeto kwenikweni kwa madera a kumpoto.+ Yesaya 14:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndikwera pamwamba pamalo okwezeka a m’mitambo.+ Ndidzipanga kukhala wofanana ndi Wam’mwambamwamba.’+
13 Iweyo wanena mumtima mwako kuti, ‘Ndikwera kumwamba.+ Ndikweza mpando wanga wachifumu+ pamwamba pa nyenyezi+ za Mulungu. Ndikhala paphiri lokumanapo+ kumapeto kwenikweni kwa madera a kumpoto.+
14 Ndikwera pamwamba pamalo okwezeka a m’mitambo.+ Ndidzipanga kukhala wofanana ndi Wam’mwambamwamba.’+