Salimo 7:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndidzatamanda Yehova chifukwa cha chilungamo chake.+Ndidzaimba nyimbo motsatizana ndi zipangizo zoimbira, kutamanda dzina+ la Yehova Wam’mwambamwamba.+ Salimo 92:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 92 Ndi bwino kuyamika inu Yehova,+Ndi kuimba nyimbo zotamanda dzina lanu, inu Wam’mwambamwamba.+
17 Ndidzatamanda Yehova chifukwa cha chilungamo chake.+Ndidzaimba nyimbo motsatizana ndi zipangizo zoimbira, kutamanda dzina+ la Yehova Wam’mwambamwamba.+