Salimo 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yehova ndi Mfumu mpaka kalekale, ndithu mpaka muyaya.+Mitundu yatheratu padziko lapansi.+ Danieli 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Zizindikiro zake n’zazikulu ndipo zodabwitsa zake n’zamphamvu.+ Ufumu wake udzakhalapo mpaka kalekale+ ndipo ulamuliro wake udzakhalapo ku mibadwomibadwo.+ Mika 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anthu amene anali kuyenda motsimphina ndidzawasonkhanitsanso pamodzi monga anthu otsala.+ Anthu amene anawachotsa m’dziko lawo ndi kuwapititsa kutali ndidzawasandutsa mtundu wamphamvu.+ Yehova adzawalamulira monga mfumu m’phiri la Ziyoni kuyambira nthawi imeneyo mpaka kalekale.+
3 Zizindikiro zake n’zazikulu ndipo zodabwitsa zake n’zamphamvu.+ Ufumu wake udzakhalapo mpaka kalekale+ ndipo ulamuliro wake udzakhalapo ku mibadwomibadwo.+
7 Anthu amene anali kuyenda motsimphina ndidzawasonkhanitsanso pamodzi monga anthu otsala.+ Anthu amene anawachotsa m’dziko lawo ndi kuwapititsa kutali ndidzawasandutsa mtundu wamphamvu.+ Yehova adzawalamulira monga mfumu m’phiri la Ziyoni kuyambira nthawi imeneyo mpaka kalekale.+