Genesis 41:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kutacha m’mawa, Farao anavutika kwambiri ndi maganizo.+ Chotero anaitanitsa ansembe onse amatsenga+ ndi amuna anzeru+ onse a mu Iguputo, n’kuwafotokozera maloto akewo.+ Koma palibe amene anatha kum’masulira Farao malotowo. Danieli 2:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Danieli anayankha mfumuyo kuti: “Chinsinsi chimene inu mfumu mukufuna kudziwa, amuna anzeru, anthu olankhula ndi mizimu, ansembe ochita zamatsenga ndi anthu okhulupirira nyenyezi, alephera kukuuzani.+ Danieli 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Chotero ansembe ochita zamatsenga, anthu olankhula ndi mizimu, Akasidi*+ ndi okhulupirira nyenyezi+ anabwera kwa ine ndipo ndinawauza malotowo, koma iwo sanathe kuwamasulira.+
8 Kutacha m’mawa, Farao anavutika kwambiri ndi maganizo.+ Chotero anaitanitsa ansembe onse amatsenga+ ndi amuna anzeru+ onse a mu Iguputo, n’kuwafotokozera maloto akewo.+ Koma palibe amene anatha kum’masulira Farao malotowo.
27 Danieli anayankha mfumuyo kuti: “Chinsinsi chimene inu mfumu mukufuna kudziwa, amuna anzeru, anthu olankhula ndi mizimu, ansembe ochita zamatsenga ndi anthu okhulupirira nyenyezi, alephera kukuuzani.+
7 “Chotero ansembe ochita zamatsenga, anthu olankhula ndi mizimu, Akasidi*+ ndi okhulupirira nyenyezi+ anabwera kwa ine ndipo ndinawauza malotowo, koma iwo sanathe kuwamasulira.+