Yobu 31:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye adzandiyeza pasikelo zolondola,+Ndipo Mulungu adzadziwa kuti ndili ndi mtima wosagawanika.+ Aroma 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye adzaweruza aliyense malinga ndi ntchito zake motere:+ 1 Akorinto 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 ntchito ya wina aliyense idzaonekera. Pakuti tsikulo lidzasonyeza ntchitoyo poyera, chifukwa moto ndiwo udzaonetsa zimenezo poyera,+ ndipo motowo udzaonetsa kuti ntchito ya munthu aliyense ndi yotani. Akolose 3:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndithudi, amene akuchita zolakwa adzalandiranso+ zolakwa zake zimene akuchitazo, chifukwa Mulungu sakondera.+
13 ntchito ya wina aliyense idzaonekera. Pakuti tsikulo lidzasonyeza ntchitoyo poyera, chifukwa moto ndiwo udzaonetsa zimenezo poyera,+ ndipo motowo udzaonetsa kuti ntchito ya munthu aliyense ndi yotani.
25 Ndithudi, amene akuchita zolakwa adzalandiranso+ zolakwa zake zimene akuchitazo, chifukwa Mulungu sakondera.+