Aroma 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye adzaweruza aliyense malinga ndi ntchito zake motere:+ 1 Akorinto 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho wobzala ndi wothirira ali amodzi,+ koma aliyense payekha adzalandira mphoto yake mogwirizana ndi ntchito yake.+ Agalatiya 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Musanyengedwe,+ Mulungu sapusitsika.+ Chilichonse chimene munthu wafesa, adzakololanso chomwecho.+
8 Choncho wobzala ndi wothirira ali amodzi,+ koma aliyense payekha adzalandira mphoto yake mogwirizana ndi ntchito yake.+