Yesaya 59:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Chilungamo tinachikankhira m’mbuyo,+ ndipo chilungamocho chinakangoima patali.+ Pakuti choonadi chapunthwa ngakhale m’bwalo la mumzinda, ndipo zinthu zolungama zikulephera kulowamo.+
14 Chilungamo tinachikankhira m’mbuyo,+ ndipo chilungamocho chinakangoima patali.+ Pakuti choonadi chapunthwa ngakhale m’bwalo la mumzinda, ndipo zinthu zolungama zikulephera kulowamo.+