Salimo 82:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Kodi mudzaweruza mopanda chilungamo,+Ndi kukondera anthu oipa kufikira liti?+ [Seʹlah.] Habakuku 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Choncho lamulo latha mphamvu ndipo anthu sakuchitanso chilungamo.+ Chilungamo chapotozedwa chifukwa anthu oipa akupondereza anthu olungama.+
4 “Choncho lamulo latha mphamvu ndipo anthu sakuchitanso chilungamo.+ Chilungamo chapotozedwa chifukwa anthu oipa akupondereza anthu olungama.+