Yesaya 11:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chilungamo ndi kukhulupirika zidzakhala lamba wa m’chiuno mwake.+ Chivumbulutso 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakati pa zoikapo nyalezo, panali wina wooneka ngati mwana wa munthu+ atavala chovala chofika kumapazi, atamanga lamba wagolide pachifuwa.
13 Pakati pa zoikapo nyalezo, panali wina wooneka ngati mwana wa munthu+ atavala chovala chofika kumapazi, atamanga lamba wagolide pachifuwa.