-
Chivumbulutso 13:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Iwo analambira chinjoka chija chifukwa chinapatsa chilombo ulamuliro. Ndipo analambira chilombocho ndi mawu awa: “Ndani ali ngati chilombo, ndipo ndani angamenyane nacho?”
-