Danieli 10:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma kalonga+ wa ufumu wa Perisiya+ ananditsekereza+ kwa masiku 21, ndipo Mikayeli,+ mmodzi mwa akalonga aakulu+ anabwera kudzandithandiza, ndipo pa nthawi imeneyo ndinakhalabe pafupi ndi mafumu a Perisiya.+
13 Koma kalonga+ wa ufumu wa Perisiya+ ananditsekereza+ kwa masiku 21, ndipo Mikayeli,+ mmodzi mwa akalonga aakulu+ anabwera kudzandithandiza, ndipo pa nthawi imeneyo ndinakhalabe pafupi ndi mafumu a Perisiya.+