Danieli 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Pambuyo pa zimenezi, ndinaona chilombo china chooneka ngati kambuku*+ koma chinali ndi mapiko anayi a mbalame pamsana pake. Chilombochi chinali ndi mitu inayi+ ndipo chinapatsidwa ulamuliro. Danieli 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mbuzi yamphongoyo inali kudzitama mopitirira muyezo,+ koma itangokhala yamphamvu, nyanga yake yaikulu inathyoledwa. Pamalo pake panamera nyanga zinayi zoonekera patali zoloza kumphepo zinayi zakumwamba.+ Danieli 8:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Popeza nyangayi inathyoka ndipo panamera zina zinayi,+ pali maufumu anayi amene adzauke mu mtundu wake, koma sadzakhala ndi mphamvu ngati zake.
6 “Pambuyo pa zimenezi, ndinaona chilombo china chooneka ngati kambuku*+ koma chinali ndi mapiko anayi a mbalame pamsana pake. Chilombochi chinali ndi mitu inayi+ ndipo chinapatsidwa ulamuliro.
8 Mbuzi yamphongoyo inali kudzitama mopitirira muyezo,+ koma itangokhala yamphamvu, nyanga yake yaikulu inathyoledwa. Pamalo pake panamera nyanga zinayi zoonekera patali zoloza kumphepo zinayi zakumwamba.+
22 Popeza nyangayi inathyoka ndipo panamera zina zinayi,+ pali maufumu anayi amene adzauke mu mtundu wake, koma sadzakhala ndi mphamvu ngati zake.