Danieli 2:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 “Pambuyo panu padzabwera ufumu wina+ wotsikirapo kwa inu.+ Kenako padzabweranso ufumu wina wachitatu, wamkuwa, umene udzalamulira dziko lonse lapansi.+ Danieli 8:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pamene ndinali kuganizira zimenezi, ndinangoona mbuzi yamphongo+ ikuchokera kolowera dzuwa kudutsa padziko lonse lapansi koma sinali kukhudza pansi. Pakati pa maso a mbuziyo panali nyanga yoonekera patali.+ Danieli 10:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Choncho iye anandiuza kuti: “Kodi ukudziwadi kuti n’chifukwa chiyani ndabwera kwa iwe? Tsopano ndibwerera kuti ndikamenyane ndi kalonga wa Perisiya.+ Pamene ndikupita, nayenso kalonga wa Girisi akubwera.+ Danieli 11:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Ndiyeno mfumu yamphamvu idzauka ndi kulamulira ndi mphamvu zazikulu,+ ndipo idzachitadi zofuna zake.+
39 “Pambuyo panu padzabwera ufumu wina+ wotsikirapo kwa inu.+ Kenako padzabweranso ufumu wina wachitatu, wamkuwa, umene udzalamulira dziko lonse lapansi.+
5 Pamene ndinali kuganizira zimenezi, ndinangoona mbuzi yamphongo+ ikuchokera kolowera dzuwa kudutsa padziko lonse lapansi koma sinali kukhudza pansi. Pakati pa maso a mbuziyo panali nyanga yoonekera patali.+
20 Choncho iye anandiuza kuti: “Kodi ukudziwadi kuti n’chifukwa chiyani ndabwera kwa iwe? Tsopano ndibwerera kuti ndikamenyane ndi kalonga wa Perisiya.+ Pamene ndikupita, nayenso kalonga wa Girisi akubwera.+
3 “Ndiyeno mfumu yamphamvu idzauka ndi kulamulira ndi mphamvu zazikulu,+ ndipo idzachitadi zofuna zake.+