2 Samueli 14:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Tsopano mu Isiraeli yense munalibe mwamuna wina wotamandika kwambiri koposa Abisalomu chifukwa cha kukongola kwake.+ Iye analibe chilema chilichonse kuyambira kuphazi mpaka paliwombo. Nyimbo ya Solomo 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Ndiwe wokongola paliponse,+ wokondedwa wanga, ndipo mwa iwe mulibe chilema chilichonse.+
25 Tsopano mu Isiraeli yense munalibe mwamuna wina wotamandika kwambiri koposa Abisalomu chifukwa cha kukongola kwake.+ Iye analibe chilema chilichonse kuyambira kuphazi mpaka paliwombo.