1 Samueli 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iyeyu anali ndi mwana wamwamuna dzina lake Sauli,+ mnyamata wokongola, ndipo panalibe munthu wina mwa ana a Isiraeli wokongola ngati iyeyu. Sauli anali wam’tali kwambiri moti panalibe munthu aliyense amene anali kum’pitirira m’mapewa ake.+
2 Iyeyu anali ndi mwana wamwamuna dzina lake Sauli,+ mnyamata wokongola, ndipo panalibe munthu wina mwa ana a Isiraeli wokongola ngati iyeyu. Sauli anali wam’tali kwambiri moti panalibe munthu aliyense amene anali kum’pitirira m’mapewa ake.+