Yeremiya 2:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Iwo akuuza mtengo kuti, ‘Ndinu bambo anga,’+ ndipo akuuza mwala kuti, ‘Ndinu amene munandibereka.’ Iwo andifulatira ndipo sanandisonyeze nkhope yawo.+ Koma tsoka likadzawagwera adzanena kuti, ‘Chonde, bwerani mudzatipulumutse!’+ Habakuku 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “‘Tsoka kwa munthu amene akuuza chidutswa cha mtengo kuti: “Dzuka!” Amene amauzanso mwala wosalankhula kuti: “Dzuka! Tipatse malangizo”!+ Taona! Fanolo ndi lokutidwa ndi golide ndi siliva+ ndipo mulibe mpweya* mkati mwake.+
27 Iwo akuuza mtengo kuti, ‘Ndinu bambo anga,’+ ndipo akuuza mwala kuti, ‘Ndinu amene munandibereka.’ Iwo andifulatira ndipo sanandisonyeze nkhope yawo.+ Koma tsoka likadzawagwera adzanena kuti, ‘Chonde, bwerani mudzatipulumutse!’+
19 “‘Tsoka kwa munthu amene akuuza chidutswa cha mtengo kuti: “Dzuka!” Amene amauzanso mwala wosalankhula kuti: “Dzuka! Tipatse malangizo”!+ Taona! Fanolo ndi lokutidwa ndi golide ndi siliva+ ndipo mulibe mpweya* mkati mwake.+