Hoseya 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iwo adzadya koma sadzakhuta.+ Adzachita zachiwerewere ndi akazi koma sadzachulukana+ chifukwa chakuti asiya kumvera Yehova.+
10 Iwo adzadya koma sadzakhuta.+ Adzachita zachiwerewere ndi akazi koma sadzachulukana+ chifukwa chakuti asiya kumvera Yehova.+