Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 24:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 M’kupita kwa nthawi iwo anasiya nyumba ya Yehova Mulungu wa makolo awo n’kuyamba kutumikira mizati yopatulika+ ndiponso mafano.+ Chotero mkwiyo wa Mulungu unagwera Yuda ndi Yerusalemu chifukwa cha kupalamula kwawoko.+

  • Salimo 125:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Koma anthu obwerera kunjira zawo zokhotakhota,+

      Yehova adzawapereka ku chilango pamodzi ndi ochita zopweteka anzawo.+

      Ndipo mu Isiraeli mudzakhala mtendere.+

  • Ezekieli 18:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 “‘Munthu wolungama akasiya chilungamo chake n’kumachita zinthu zopanda chilungamo,+ akamachita zopanda chilungamo+ n’kumakhalabe ndi moyo, zinthu zolungama zonse zimene anachita sizidzakumbukiridwa.+ Iye adzafa chifukwa chochita zinthu mosakhulupirika ndiponso chifukwa cha machimo ake amene anachita.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena