1 Samueli 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsopano ana aamuna a Eli anali anthu opanda pake.+ Iwo anali kunyalanyaza Yehova.+ Yeremiya 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Iwe wakhala pakati pa chinyengo.+ Chifukwa cha chinyengo chawo akana kundidziwa ine,”+ watero Yehova.
6 “Iwe wakhala pakati pa chinyengo.+ Chifukwa cha chinyengo chawo akana kundidziwa ine,”+ watero Yehova.