Malaki 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yuda wachita zachinyengo, ndipo mu Isiraeli ndi mu Yerusalemu mwachitika zinthu zonyansa.+ Pakuti Yuda wadetsa chiyero cha Yehova+ chimene Mulungu amachikonda, ndipo Yuda wakwatira mwana wamkazi wa mulungu wachilendo.+
11 Yuda wachita zachinyengo, ndipo mu Isiraeli ndi mu Yerusalemu mwachitika zinthu zonyansa.+ Pakuti Yuda wadetsa chiyero cha Yehova+ chimene Mulungu amachikonda, ndipo Yuda wakwatira mwana wamkazi wa mulungu wachilendo.+