3 Usadzachite nawo mgwirizano wa ukwati. Usadzapereke ana ako aakazi kwa ana awo aamuna ndipo usadzatenge ana awo aakazi ndi kuwapereka kwa ana ako aamuna.+
6 Aisiraeli anatenga ana aakazi a Akanani kukhala akazi awo,+ ndipo ana awo aakazi anawapereka kwa ana aamuna a Akanani,+ moti Aisiraeli anayamba kutumikira milungu ya Akanani.+