Miyambo 15:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Aliyense wokana malangizo+ amakana moyo wake, koma munthu womvetsera chidzudzulo amakhala ndi mtima wanzeru.+ Yesaya 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ng’ombe yamphongo imam’dziwa bwino munthu amene anaigula, ndipo bulu amadziwa chinthu chimene mbuye wake amam’dyetseramo. Koma Isiraeli sandidziwa,+ ndipo anthu anga sanachite zinthu mozindikira.”+
32 Aliyense wokana malangizo+ amakana moyo wake, koma munthu womvetsera chidzudzulo amakhala ndi mtima wanzeru.+
3 Ng’ombe yamphongo imam’dziwa bwino munthu amene anaigula, ndipo bulu amadziwa chinthu chimene mbuye wake amam’dyetseramo. Koma Isiraeli sandidziwa,+ ndipo anthu anga sanachite zinthu mozindikira.”+