Yobu 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Malinga ndi zimene ine ndaona, anthu okonzera anzawo zopweteka,Ndi ofesa mavuto, amakolola zomwezo.+ Miyambo 22:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Wofesa zosalungama adzakolola zopweteka,+ ndipo ndodo ya ukali wake idzatha.+ Agalatiya 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Musanyengedwe,+ Mulungu sapusitsika.+ Chilichonse chimene munthu wafesa, adzakololanso chomwecho.+
8 Malinga ndi zimene ine ndaona, anthu okonzera anzawo zopweteka,Ndi ofesa mavuto, amakolola zomwezo.+