Salimo 33:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Palibe mfumu imene inapulumuka chifukwa cha kukula kwa gulu lake lankhondo.+Munthu wamphamvu sapulumuka chifukwa cha kuchuluka kwa mphamvu zake.+ Salimo 146:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Musamakhulupirire anthu olemekezeka,+Kapena mwana wa munthu wina aliyense wochokera kufumbi amene alibe chipulumutso.+ Yeremiya 17:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova wanena kuti: “Wotembereredwa ndi munthu aliyense wokhulupirira mwa munthu aliyense wochokera kufumbi.+ Wotembereredwa ndi munthu amene amadalira mphamvu za dzanja la munthu,+ komanso amene mtima wake wapatuka kuchoka kwa Yehova.+
16 Palibe mfumu imene inapulumuka chifukwa cha kukula kwa gulu lake lankhondo.+Munthu wamphamvu sapulumuka chifukwa cha kuchuluka kwa mphamvu zake.+
3 Musamakhulupirire anthu olemekezeka,+Kapena mwana wa munthu wina aliyense wochokera kufumbi amene alibe chipulumutso.+
5 Yehova wanena kuti: “Wotembereredwa ndi munthu aliyense wokhulupirira mwa munthu aliyense wochokera kufumbi.+ Wotembereredwa ndi munthu amene amadalira mphamvu za dzanja la munthu,+ komanso amene mtima wake wapatuka kuchoka kwa Yehova.+