Salimo 62:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndithudi, ana a anthu ochokera kufumbi ali ngati mpweya,+Ana a anthu ndi malo othawirako achinyengo.+Onse pamodzi akaikidwa pasikelo ndi opepuka kuposa mpweya.+ Salimo 118:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kuthawira kwa Yehova n’kwabwino+Kusiyana ndi kudalira anthu olemekezeka.+
9 Ndithudi, ana a anthu ochokera kufumbi ali ngati mpweya,+Ana a anthu ndi malo othawirako achinyengo.+Onse pamodzi akaikidwa pasikelo ndi opepuka kuposa mpweya.+