2 Samueli 15:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Kenako uthenga unafika kwa Davide wonena kuti: “Ahitofeli nayenso ali pakati pa anthu amene akukonza chiwembu+ pamodzi ndi Abisalomu.”+ Pamenepo Davide anati:+ “Inu Yehova!+ Chonde, sandutsani malangizo a Ahitofeli kuti akhale opusa.”+ Salimo 60:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tithandizeni kuti tichoke m’masautso,+Pakuti chipulumutso chochokera kwa munthu wochokera kufumbi n’chopanda pake.+ Aroma 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ayi! Koma Mulungu akhale wonena zoona,+ ngakhale kuti munthu aliyense angapezeke kukhala wonama,+ monganso Malemba amanenera kuti: “Mukamalankhula mumalankhula zachilungamo, kuti mupambane pamene mukuweruzidwa.”+
31 Kenako uthenga unafika kwa Davide wonena kuti: “Ahitofeli nayenso ali pakati pa anthu amene akukonza chiwembu+ pamodzi ndi Abisalomu.”+ Pamenepo Davide anati:+ “Inu Yehova!+ Chonde, sandutsani malangizo a Ahitofeli kuti akhale opusa.”+
11 Tithandizeni kuti tichoke m’masautso,+Pakuti chipulumutso chochokera kwa munthu wochokera kufumbi n’chopanda pake.+
4 Ayi! Koma Mulungu akhale wonena zoona,+ ngakhale kuti munthu aliyense angapezeke kukhala wonama,+ monganso Malemba amanenera kuti: “Mukamalankhula mumalankhula zachilungamo, kuti mupambane pamene mukuweruzidwa.”+