Yesaya 30:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 amene akupita ku Iguputo+ osafunsira kwa ine,+ ndiponso amene akupita ku Iguputo kuti akapeze chitetezo kwa Farao ndi kukabisala mumthunzi wa Iguputo.+ Ezekieli 29:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Atakugwira dzanja ndi kukutsamira ngati ndodo yoyendera, unaphwanyika+ ndipo unachititsa kuti miyendo* yawo ikhale yagwedegwede,+ zimene zinawachititsa kuti athyole+ phewa lawo.”
2 amene akupita ku Iguputo+ osafunsira kwa ine,+ ndiponso amene akupita ku Iguputo kuti akapeze chitetezo kwa Farao ndi kukabisala mumthunzi wa Iguputo.+
7 Atakugwira dzanja ndi kukutsamira ngati ndodo yoyendera, unaphwanyika+ ndipo unachititsa kuti miyendo* yawo ikhale yagwedegwede,+ zimene zinawachititsa kuti athyole+ phewa lawo.”