Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 17:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Koma mfumu ya Asuri inaona kuti Hoshiya anali kuichitira chiwembu,+ chifukwa chakuti iye anatumiza amithenga kwa So mfumu ya Iguputo,+ ndiponso sanapereke msonkho kwa mfumu ya Asuri monga anali kuchitira zaka zam’mbuyo. Choncho mfumu ya Asuri inam’manga n’kumutsekera m’ndende.+

  • Yesaya 31:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Tsoka kwa anthu amene akupita ku Iguputo kukapempha thandizo.+ Iwo akudalira mahatchi wamba+ ndi kukhulupirira magaleta ankhondo,+ chifukwa chakuti ndi ambiri. Akudaliranso mahatchi akuluakulu chifukwa chakuti ndi amphamvu kwambiri, koma sanayang’ane kwa Woyera wa Isiraeli ndipo sanafunefune Yehova.+

  • Ezekieli 29:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Anthu onse okhala ku Iguputo adzadziwa kuti ine ndine Yehova+ chifukwa chakuti iwo anali ngati bango loyendera la nyumba ya Isiraeli.+

  • Hoseya 7:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Efuraimu ali ngati nkhunda yopusa,+ yopanda nzeru.+ Iwo apempha thandizo ku Iguputo+ ndiponso apita kudziko la Asuri.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena