Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 9:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Anthuwo sanabwerere kwa amene akuwamenya+ ndipo sanafunefune Yehova wa makamu,+

  • Yesaya 64:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Palibe amene akutamanda dzina lanu.+ Palibe amene akutekeseka kuti akufunefuneni ndi kukugwirani mwamphamvu, pakuti mwatibisira nkhope yanu+ ndipo mwatichititsa kuti tisungunuke+ ndi mphamvu ya zolakwa zathu.

  • Danieli 9:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Masoka onse amene analembedwa m’chilamulo cha Mose+ atigwera,+ ndipo ife sitinakhazike pansi mtima wanu, inu Yehova Mulungu wathu, mwa kusiya zolakwa zathu+ ndi kusonyeza kuti tikumvetsa kuti ndinu wokhulupirika.+

  • Hoseya 7:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Onsewo akutentha ngati ng’anjo yamoto, ndipo akuwononga oweruza awo. Mafumu awo onse agwa.+ Palibe aliyense wa iwo amene akundiitana.+

  • Amosi 5:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 “Yehova wauza anthu a m’nyumba ya Isiraeli kuti, ‘Yesetsani kundiyandikira,+ kuti mupitirize kukhala ndi moyo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena