2 Mafumu 24:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 M’masiku ake, Nebukadinezara+ mfumu ya Babulo anabwera kudzachita nkhondo ndi Yerusalemu. Choncho Yehoyakimu anakhala mtumiki wake+ kwa zaka zitatu, koma kenako anam’pandukira. 2 Mafumu 24:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Zimene zinachitika ku Yerusalemu ndi ku Yuda zinakwiyitsa+ kwambiri Yehova ndipo anawachotsa pamaso pake.+ Kenako Zedekiya anapandukira mfumu ya Babulo.+ Ezekieli 17:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma iye anapandukira+ mfumuyo potumiza amithenga ku Iguputo kuti dziko la Iguputo limupatse mahatchi*+ ndi khamu la anthu. Kodi zinthu zidzamuyendera bwino? Kodi munthu amene akuchita zinthu zimenezi ndiponso amene akuphwanya pangano adzapulumuka? Kodi iye adzapulumukadi?’+
24 M’masiku ake, Nebukadinezara+ mfumu ya Babulo anabwera kudzachita nkhondo ndi Yerusalemu. Choncho Yehoyakimu anakhala mtumiki wake+ kwa zaka zitatu, koma kenako anam’pandukira.
20 Zimene zinachitika ku Yerusalemu ndi ku Yuda zinakwiyitsa+ kwambiri Yehova ndipo anawachotsa pamaso pake.+ Kenako Zedekiya anapandukira mfumu ya Babulo.+
15 Koma iye anapandukira+ mfumuyo potumiza amithenga ku Iguputo kuti dziko la Iguputo limupatse mahatchi*+ ndi khamu la anthu. Kodi zinthu zidzamuyendera bwino? Kodi munthu amene akuchita zinthu zimenezi ndiponso amene akuphwanya pangano adzapulumuka? Kodi iye adzapulumukadi?’+