Yobu 3:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 N’chifukwa chiyani Mulungu amapereka kuwala kwa mwamuna wamphamvu amene njira yake yabisika,+Amene Mulungu akum’pingapinga?+ Maliro 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Wanditsekereza ngati mmene mpanda wamiyala umatsekerezera, kuti ndisatuluke.+ Wandimanga ndi maunyolo olemera amkuwa.+
23 N’chifukwa chiyani Mulungu amapereka kuwala kwa mwamuna wamphamvu amene njira yake yabisika,+Amene Mulungu akum’pingapinga?+
7 Wanditsekereza ngati mmene mpanda wamiyala umatsekerezera, kuti ndisatuluke.+ Wandimanga ndi maunyolo olemera amkuwa.+